Anthu okhala pa zilumba za Likoma ndi Chizumulu pakali pano ali ndi mwayi oyenda mosavuta kuchokera pa zilumbazo kufika ku Nkhata-Bay ndi madera ena pomwe Unduna wa za Mtengatenga ndi zomangamanga wati Sitima ya MV Chambo yomwe inalembetsedwa mukaundula wa Sitima ku dziko la Mozambiki iyambilenso kuyenda pa nyanja ya Malawi. M'neneri mu undunawu Watson […]
The post Sitima ya MV Chambo ikuyambiranso maulendo ake pa Nyanja ya Malawi appeared first on Malawi 24.