Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati boma lalandira mayankho opatsa chilimbikitso pa nkhani ya kafukufuku wa ngozi yomwe inakhudza wachiwiri wa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima ndi ena asanu ndi atatu. Poyankhura pa msonkhano wa atolankhani lero ku Lilongwe, a Kunkuyu ati zinthu zambiri zokhudza tsatane tsatane wa kafukufuku yemwe akuyembekerezedwayu afotokozerabe […]
The post Talandira mayankho opatsa chilimbikitso pa nkhani ya kafukufuku - Kunkuyu appeared first on Malawi 24.