Thupi la katswiri pa mayimbidwe, Lucius Banda, likuyembekezeka kufika m’dziko muno lero masanawa kuchokera m'dziko la South Africa komwe wamwalilira, ndipo pali chiyembekezo kuti lilowa m’manda Lachinayi sabata ino. Izi ndi malingana ndi mwana wa malemu Banda, Benson yemwe wauza nyumba zina zowulutsira mawu m’dziko muno kuti thupi la malemu bambo ake lifika m'dziko muno […]
The post Thupi la Lucius Banda lifika m’dziko muno masanawa appeared first on Malawi 24.