Ngati muli ndi zithuzi zomwe munajambula zakudya zomwe munaphika nokha ndipo zimaoneka mopatsa mudyo, pansi mtedza; kunjaku kuli Crossroads Hotel (Blantyre) yomwe yayaluka kamba kotenga zithuzi za zakudya zophikidwa kwina mkumati zaphikidwa kwawoko. Chatsitsa dzaye kuti njovu ithyoke nyanga nchakuti, Lolemba pa 22 April, 2024, tsamba la fesibuku la wayilesi ya Zodiak panaikidwa chithuzi choitanira […]
The post Tsiku la 40: Crossroads Hotel yagwidwa ndi zithuzi za zakudya zomwe siinaphike ndiiyo appeared first on Malawi 24.