Apolisi ku Chitipi m'boma la Lilongwe amanga mayi wina wa zaka 24 kamba komuganizira kuti wapha mamuna wake a Misheck Byson powakoka maliseche. M'neneli wa apolisi m’bomali a Sub Inspector Hastings Chigalu, atsimikizira za nkhaniyi ndipo ati mayiyu ndi Ruth Nkhoma. Malingana ndi a Chigalu, ati pa 17 June mwezi uno awiriwa adakangana pankhani yokhudza […]
The post Wapha mamuna wake atamukoka maliseche appeared first on Malawi 24.