Achinyamata okwana 500 ndi omwe akuyembekezeka kunyamuka mwezi wa mawa kupita kukagwira tchito mdziko la Israel. Mmodzi mwa akuluakulu ku unduna wa za ntchito a Paul Kalilombe wauza komiti ya Public Accounts ku nyumba ya malamulo kuti izi zili chonchi molingana ndi zomwe maiko a Malawi ndi Israel adakambirana posachedwapa. Iwo ati boma lapatsidwa mwayi oti […]
The post Wapsa waku Israel: Achinyamata 500 anyamuka mu mwezi wa August appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.