…owina tsopano azitenga MK100 miliyoni…yonse pamodzi yafika pa MK500 miliyoni Koma apambane ligi chaka chino adya bwino. Yamasula ma bureki TNM, chithumba cha ligi angokhuthula. Malonjezo a Fleetwood Haiya mmbalimo akukwanitsidwa. Atayamba mokhala ngati akusisitika, kampani ya TNM lero yamwetsa Mkaka anthu okonda masewero mu dziko muno italengeza kuti tsopano yakweza ndalama zimene imapereka ku […]
The post Wayamba kukwaniritsa malonjezo Haiya: chithumba cha ligi chakwera appeared first on Malawi 24.