Ubale omwe unayamba zaka zitatu zapitazo pakati pa timu ya Mighty Wanderers ndi kampani ya Mukuru wathapo tsopano. Mu kalata yomwe Wanderers yatulutsa yomwe watsimikiza ndi mlembi wa board ya timuyi, a Chancy Gondwe komanso wamkuru owona za malonda ku kampani ya Mukuru, a Brandon Mncube ati, ubalewu wazilalapo awiriwa atagwirizana kusayenderanso limodzi. 'Mbali ziwirizi […]
The post Zathapo, Wanderers ndi Mukuru alekana appeared first on Malawi 24.