Kutsatira kusefukira kwa madzi komwe kwakhudza anthu m'boma la Dowa ku Mponela, bungwe loona za ngozi zogwa mwadzidzidzi la DODMA dzulo lapereka thandizo losiyasiyana kuphatikizapo ufa, mabulangete, mabigiri, matenti, komanso nyemba. Bungweli lapereka mabulangete okwana 139, ufa matumba okwana 37, nyemba zolemera ma kilogiramu 10 kubanja lililonse, matenti, komanso ma mabigiri okwana 37. A Mercy […]
The post DODMA yapereka thandizo kwa anthu okhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi ku la Dowa appeared first on Malawi 24.