Phungu wa ku nyumba ya malamulo m'dera la Chikwawa Nkombezi, Abida Mia, abwera poyera kuti akapikisana nawo pa mpando wa wachiwiri kwa wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Malawi Congress (MCP) pansonkhano waukulu wachipani omwe uchitike mwezi wa mawa wa August. Polankhula ndi Malawi24 a Mia omwenso ndi nduna ya za madzi ndi ukhondo ati […]
The post Abida Mia akapikisana nawo pampando wa wachiwiri kwa wachiwiri kwa mtsogoleri wachipani cha MCP appeared first on Malawi 24.