Login to BlackFacts.com using your favorite Social Media Login. Click the appropriate button below and you will be redirected to your Social Media Website for confirmation and then back to Blackfacts.com once successful.
Enter the email address and password you used to join BlackFacts.com. If you cannot remember your login information, click the “Forgot Password” link to reset your password.
Pali kuthekera kwakukulu kuti anthu ena omwe angolowa kumene chipani cha Malawi Congress (MCP) sakapikisana nawo ku msonkhano waukulu wachipani-chi pamene komiti yomwe ikuyendetsa msonkhanowu ikuwunikira zikalata za opikisana. Anthu omwe awonetsa chidwi kukapikisana nawo pa maudindo osiyana-siyana apereka zikalata zawo, koma komiti ikuwunika pofuna kupeza omwe ali ovomerezeka. Nkhalapampando wakomiti yomwe ikuyendetsa zokonzekera za […]
The post Ena aletsedwa kuyima ku konveshoni ya MCP appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.
Sorry that there are no other Black Facts here yet!
This Black Fact has passed our initial approval process but has not yet been processed by our AI systems yet.
Once it is, then Black Facts that are related to the one above will appear here.