Zadziwika kuti mayunitsi a lamya okhala pa khadi lija limachita kukalidwa lija, akhala akuthetsedwa mdziko muno sabata ya mawa ino. Izi zikutsatira mikumano yomva maganizo a anthu yomwe bungwe lowona za nkhani zolumikizana la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) lakhala likuchititsa mbuyomu pa nkhaniyi. Potsatira nkhaniyi, bungweli laitanitsa msonkhano wa atolankhani omwe uchitike pa 30 […]
The post Mayunitsi okala akuthetsedwa m’dziko muno appeared first on Malawi 24.