Pomwe anthu akupitilirabe kusonkha ndalama zokwana 43 miliyoni kuti thupi la malemu Hope Chisanu lifike kuno, anthu m’dziko la America atsazikana ndi malemuyu kumapeto a mwezi uno. Chisanu yemwe wasiya mkazi ndi ana awiri, anamwalira Loweluka pa 1 June 2024 atadwala kwa nthawi yochepa m’dziko la America komwe amakhala. Potsatira imfayi, akubanja anakhazikitsa ntchito yosonkhetsa […]
The post Mwambo wa maliro a Hope Chisanu uchitika mwezi uno ku America appeared first on Malawi 24.