Mzibambo wa zaka 21 zakubadwa, wagamulidwa kukagwira ukaidi kwa zaka zisanu kamba kobaya mayi wake woyembekezera ndikupha mwana yemwe amayemnekezeredwayo. Malingana ndi woyimilira boma pa mulanduwu a Mussa Samuteni, mzibambo wopanda chisoniyu yemwe wazindikilidwa kuti ndi Happy Banda, wamangidwa posachedwapa atabaya mayi wake woyembekezerawa ndi mpeni pamimba. Izi zapangitsa kuti bwalo la milandu la Nkhunga […]
The post Mzibambo obaya mayi ake oyembekezera akaseweza jere appeared first on Malawi 24.