Mnyamata wa zaka 23, Chikondi Maluwa amugamula kuti akagwire jere kwa zaka zitatu, bwalo la milandu la Midima ku Limbe mu mzinda wa Blantyre litamupeza olakwa pa mulandu okuba Ng'ombe ya Eid. Malingana ndi ofalitsa nkhani za polisi ya Limbe, a Aubrey Singanyama ati ogamulidwayu anaba Ng'ombeyo yomwe inali ya Eid ku Mpingwe mu mzinda […]
The post Ng'ombe ya eid yakankhira mnyamata ku ndende appeared first on Malawi 24.