Bwalo lalikulu lozenga milandu ku Mzuzu lathetsa mlandu omwe limamuzenga Tadikira Mafubza Mutharika komanso anthu ena asanu ndi awiri. Tadikira yemwe ndi mwana wa a Gertrude Mutharika anamangidwa pamodzi ndi anthu asanu ndi awiriwa powaganizira kuti anatengapo gawo pa milandu yozembetsa komanso kupha anthu makumi atatu omwe amaganizilidwa kuti ndi nzika za dziko la Ethiopia […]
The post Tadikira tsopano ndi mfulu appeared first on Malawi 24.