Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika, omweso ndi mtsogoleri wa chipani cha DPP, wawuza mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera kuti asiye kuzunza anthu achigawo chakum'mwera ponena kuti iwo pokhala m'busa sakuyenera kumachita tsankho. A Mutharika amayankhula izi Lamulungu pa 19 December pa bwalo la Njamba mumzinda wa Blantyre pomwe chipani cha DPP […]
The post Abusa a Chakwera musiye kumanga anthu a kum’mwera – Mutharika appeared first on Malawi 24.